Werengani tsopano

August 2025

Kuti tilumikizane nanu polandila za malembawa ku kuomputa yanu, kapena pa foni


ZIMENE TIKUKHULUPIRIRA

  • Baibulo ndi vumbulutso la cholinga cha Mulungu choperekedwa kudzera mwa anthu anzeru amene amatsogozedwa ndi Mzimu Wake, choncho ndi losalephera komanso lamphamvu.
  • Baibulo limasonyeza kuti Mulungu ndi Mlengi ndiponso Wosamalira zinthu zonse. Iye amakhala kumwamba m’kuunika kosafikirika. Iye ndi wamphamvu yonse, wanzeru zonse, Mulungu wa chikondi, chifundo, chiyero, chilungamo ndi choonadi. Mulungu ndi umodzi